فِيَّ حُبٌّ فِيَّ وَجدٌ واشتياقٌ لا يُحَدُّ
يا رَسولَ اللهِ قَلبِي لم يَزَلْ بِاسْمِكَ يَشْدُو
M'mtima mwanga muli chikondi, muli chikhumbo chosadziwika malire
O Mtumiki wa Allah! Mtima wanga sunasiye kuyimba dzina lanu
أَنتَ لِلعَالَمِ رَحْمة جِئتَ تَمْحُو كُلَّ ظُلمَة
نَحْنُ يا خَيْرَ رَسولٍ بِكَ صِرْناَ خَيرَ أُمّة
Ndinu chifundo kwa dziko lonse, mudabwera kufafaniza mdima uliwonse,
O Wabwino wa Atumiki! Chifukwa cha Inu, tinasanduka Gulu Labwino
فِيَّ حُبٌّ فِيَّ وَجدٌ واشتياقٌ لا يُحَدُّ
يا رَسولَ اللهِ قَلبِي لم يَزَلْ بِاسْمِكَ يَشْدُو
M'mtima mwanga muli chikondi, muli chikhumbo chosadziwika malire
O Mtumiki wa Allah! Mtima wanga sunasiye kuyimba dzina lanu
حُبُّكَ السَاكِنُ فِيَّ لَمْ يَزَلْ يَهْمِي عَلَيَّ
بَهْجَةً فِي الرُّوحِ فَاضَتْ وَسَلاماً اَبَدِيَّ
Chikondi chanu chakhala mkati mwanga, chimapitiriza kugwera pa ine
Chisangalalo ndi Mtendere Wosatha wazaza moyo wanga!
فِيَّ حُبٌّ فِيَّ وَجدٌ واشتياقٌ لا يُحَدُّ
يا رَسولَ اللهِ قَلبِي لم يَزَلْ بِاسْمِكَ يَشْدُو
M'mtima mwanga muli chikondi, muli chikhumbo chosadziwika malire
O Mtumiki wa Allah! Mtima wanga sunasiye kuyimba dzina lanu
صَلِ يَا رَبِّ عَلَيْهِ وَاسْقِنَا مِنْ رَاحَتَيهِ
ذَابَتِ الرُّوحُ وَتَاقَت وَبَكَتْ شَوقًا إِلَيْهِ
Tumizani Madalitso Pa Iye O Mbusa wanga, tipatseni kumwa kuchokera m'manja Mwake Odalitsika
Mzimu Usungunuka ndi kulapa, ndi Kulira mu Chikhumbo cha Iye!
فِيَّ حُبٌّ فِيَّ وَجدٌ واشتياقٌ لا يُحَدُّ
يا رَسولَ اللهِ قَلبِي لم يَزَلْ بِاسْمِكَ يَشْدُو
M'mtima mwanga muli chikondi, muli chikhumbo chosadziwika malire
O Mtumiki wa Allah! Mtima wanga sunasiye kuyimba dzina lanu
مُذ دَعَا بِالنُّورِ دَاعٍ رَدَّدَتْ كُلُّ البِقَاعِ
طَلَعَ البَدْرُ عَلَيْنَا مِنْ ثَنِيَّاتِ الوَدَاعِ
Kuyambira pomwe Woyitanira adaitana ndi Kuwala Kwake Kodalitsika, Malo onse anayankha
Mwezi Wathunthu Wokongola wawuka pa ife kuchokera mu Chigwa Chodalitsika cha Wadaa