رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
Takondwa inu ana a Al-Zahra takondwa
Ny
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
رضينا بالنبيِّ لنا إمَامًا
وأنْتُم آلُهُ وبِكُمْ رَضِينَا
Takhutila ndi Mneneri kukhala Mtsogoleri wathu
ndipo inu ndinu banja lake ndipo mwa inu takhutila
وبالسِّبْطِ الحُسَيْنِ كَذَا أخُوهُ
وَحَيْدَرُ ثُمَّ زَيْنُ العَابِدِينَا
Ndi mdzukulu Husayn komanso mchimwene wake
ndi Haydar kenako Zayn al-Abidina
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
وَزَيْنَبُ مَنْ لها فَضْلٌ سَمِيٌّ
سُلاَلَةُ أَحْمَدٍ في الطَّيِّبِينَا
Ndi Zaynab amene ali ndi ulemu wapamwamba
mbadwa ya Ahmad pakati pa anthu abwino
لها نُورٌ يُضِيءُ كَمِثْلِ شَمْسٍ
من المُخْتَارِ نَشْهَدُهُ مُبِينَا
Ali ndi kuwala kowala ngati dzuwa
kochokera kwa Osankhidwa komwe tikuona mowonekera
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
لها جُودٌ لها كَرَمٌ وعَطْفٌ
حَوَتْ فَضْلاً يُرَى للمُنْصِفِينَا
Ali ndi kuwolowa manja, ulemu ndi chifundo
ali ndi ubwino woonekera kwa oweruza mwachilungamo
أمير المؤمنين أَبُوكِ حَقًّا
عَلِيٌّ سَادَ جَيْشَ العَارِفِينَا
Mtsogoleri wa Okhulupirira ndiye tate wanu ndithu
Ali amene anatsogolera asilikali a odziwa
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
وأُمُّكِ بَضْعَةُ المُخْتَارِ طَهَ
مُحَبَّبَةٌ إلى الهادي نبينا
Ndipo ama wanu ndi mbali ya Osankhidwa Taha
wokondedwa kwa Wotsogolera, Mneneri wathu
وكَانَ المُصْطَفَى يَحْنُو عَلَيْهَا
حُنُوَّ مَوَدَّةٍ عَطْفًا وَلِينَا
Ndipo Al-Mustafa anali kumuchitira chifundo
chifundo cha chikondi, kufatsa ndi kukoma mtima
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
وجَاءَ حَدِيثُهُ يُتْلَى جِهَارًا
لَقَدْ سَادَتْ نِسَاءَ العَالَمِينَا
Ndipo mau ake anafika powerengedwa poyera
kuti iye ndiye mfumu ya akazi a m’mitundu yonse
إذا اشْتَقْنَا إلى خَيْرِ البَرَايَا
أَتَيْنَاكُمْ مُشَاةً رَاكِبِينَا
Tikasowa iye amene ali wabwino mwa zolengedwa
timabwera kwa inu poyenda kapena okwera
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
فأنتم منه بالأسرار جِئْتُمْ
وَجِئْنَاكُمْ فَشَاهَدْنَا الأَمِينَا
Pakuti inu mwachokera kwa iye ndi zinsinsi
ndipo tabwera kwa inu n’kumuona Odalirika
وشَاهَدْنَا لديكم كُلَّ خَيْرٍ
وشَاهَدْنَا أُلُوفًا زَائرِينَا
Taona zabwino zonse pamaso panu
ndipo taona alendo masauzande ambiri
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
بإخْلاَصٍ وتوحيد ودِينٍ
أَتَوْكُمْ سَادَتِي مُتَبَرِّكِينَا
Ndi kudzipereka, umodzi wa Mulungu ndi chipembedzo
anabwera kwa inu, ambuye anga, kufuna mdalitso
تُذَكِّرُهُمْ مَشَاهِدُكُمْ جِنَانًا
بِرَوْضَةِ جَدِّكُمْ لِلْوَفِدِينَا
Malo anu amawakumbutsa za m’minda ya m’mwamba
m’munda wa agogo anu kwa obwera onse
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
فَرَوْحٌ مِنْهُ والرَّيْحَانُ يأتي
لِزُوَّارٍ أَتَوْكُمْ مُخْلِصِينَا
Mpweya wabwino ndi fungo lokoma limachokera kwa iye
kwa alendo amene anabwera kwa inu mowona mtima
فأنتم مِنْهُ والذِّكْرَى لَدَيْكُمْ
برُؤيَاكُمْ تُرَى للمُؤْمِنِينَا
Pakuti inu muli mbali yake ndipo chikumbutso chili ndi inu
mwa kukuonani inu, zikuoneka kwa okhulupirira
رَضِينَا يا بَنِي الزَّهْرَا رَضِينَا
بِحُبٍّ فيكُمُوا يُرْضي نَبِينَا
Takhutila inu mbadwa za Zahra takhutila
ndi chikondi pa inu chomwe chimakondweretsa Mneneri wathu
فَبَابُ العِلْمِ والدُكُمْ عَلِيٌّ
له سَيْفٌ أَبَادَ الكَافِرِينَا
Chipata cha nzeru ndi tate wanu Ali
ali ndi lupanga limene linaononga osakhulupirira
فَمِنْ دَمْعٍ لأرضٍ قد رَوَيْنَا
مِنَ الأَشْوَاقِ نَحْوَ الأَكْرَمِينَا
Ndi misozi tathirira nthaka
chifukwa cha kulakalaka kwanu inu olemekezeka