رَبِّي لَهُ الْأَسْمَاءُ الْحُسْنَى
Ambuye wanga ali ndi maina okongola koposa
Ny
رَبِّي لَهُ الْأَسْمَاءُ الْحُسْنَى
تُسَبِّحْ لَهُ الْأكْوَانْ
Ambuye wanga ali ndi Maina Okongola koposa
Chilengedwe chonse chimatamanda Iye
إِلَيْهِ يَرْجِعُ كُلُّ أَمْرٍ
كُلُّ زَمَانٍ وَكُلَّ مَكَانْ
Kwa Iye kumabwerera nkhani zonse
Nthawi iliyonse komanso malo aliyense
إِذَا دَعَوْتْ فَادْعُ الْإِلَهْ
وَإِنِ اسْتَجَرْتَ فَلُذْ بِاللَّهْ
Mukapemphera, itanani Mulungu mmodzi
Mukafuna pothawirapo, tembenukirani kwa Allah
مَا لَنَا مَوْلًى سِوَاهْ
عَفُوٌّ كَرِيمٌ وَرَحْمَانْ
Tilibe Mtetezi wina koma Iye
Wokhululukira, Wowolowa manja, ndi Wachifundo
رَبِّي لَهُ الْأَسْمَاءُ الْحُسْنَى
تُسَبِّحْ لَهُ الْأكْوَانْ
Ambuye wanga ali ndi Maina Okongola koposa
Chilengedwe chonse chimatamanda Iye
إِلَيْهِ يَرْجِعُ كُلُّ أَمْرٍ
كُلُّ زَمَانٍ وَكُلَّ مَكَانْ
Kwa Iye kumabwerera nkhani zonse
Nthawi iliyonse komanso malo aliyense
اتَّقِ اللَّهْ وَلَهُ اِصْبِرْ
فَالْصَّبْرُ فِي الْعُقْبَى حَمِيدْ
Muziopa Allah ndipo mupirire chifukwa cha Iye
Pakuti kupirira kumadzetsa mapeto otamandika
وَتَزَوَّدْ عِلْمًا وَبَيَانًا
مِنَ الْسُّنَّةِ وَالْقُرْآنْ
Dzikonzekeretseni ndi nzeru ndi kuzindikira
Kochokera mu Sunnah ndi mu Qur'an