يَا وَاهِبَ الْإِنْسَانِ أَسْبَابَ الْهُدَى
Inu Opatsa Mtundu wa Anthu Njira za Chitsogozo
Ny
يَا وَاهِبَ الْإِنْسَانِ أَسْبَابَ الْهُدَى
يَا مَنْ بِحَمْدِ الْعَالَمِينَ تَفَرَّدَا
Oh Opatsa anthu njira zachiongoko
Oh Inu amene nokha muyenera matamando a chilengedwe chonse
لِي عِنْدَ بَابِكَ يَا إِلَهِي دَعْوَةٌ
فِيهَا رَجَاءُ الْعُمْرِ جَاءَ مُجَسَّدَا
Pa khomo panu, Inu Mulungu wanga, ndili ndi pempho
Momwe chiyembekezo cha moyo wanga wonse chadzera mwa maonekedwe
أَنْتَ الَّذِي مَا خَابَ عِنْدَكَ سَائِلٌ
أَيَكُونُ بَابُكَ دُونَ سُؤْلِي مُؤْصَدَا
Inu ndinu amene wopempha sakhumudwa kwa Inu
Kodi khomo lanu lingatsekedwe pa pempho langali?
فَبِفَضْلِكَ اللَّهُمَّ عِشْتُ مُوَحِّدا
أَيُرَدُّ عِنْدَكَ مَنْ أَتَاكَ مُوَحِّدَا
Ndi chisomo chanu, Allah, ndakhala ndikuvomereza umodzi wanu
Kodi amene wadza kwa Inu akuvomereza umodzi wanu angabwezedwe?
سُؤْلِي كَذَاتِكَ وَاحِدٌ فَبِحَقِّهَا
لَوْ لَحْظَةً دَعْنِي أُشَاهِدَ أَحْمَدَا
Pempho langa ndi limodzi monga Umunthu wanu; tsono mwa umodziwo
Ngakhale kamphindi, ndiloleni ndimuone Ahmad